Machitidwe 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma chinthu chimodzi chokha chimene ndikudziwa nʼchakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti ndikuyembekezera kumangidwa komanso kuzunzidwa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:23 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 189
23 Koma chinthu chimodzi chokha chimene ndikudziwa nʼchakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti ndikuyembekezera kumangidwa komanso kuzunzidwa.+