Machitidwe 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:23 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 189
23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+