-
Machitidwe 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Titadzikakamiza nʼkusiyana nawo, tinayamba ulendo wathu wapanyanja. Tinayenda osakhota mpaka kukafika ku Ko. Tsiku lotsatira tinafika ku Rode ndipo titachoka kumeneko tinakafika ku Patara.
-