Machitidwe 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chilumba cha Kupuro chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere* nʼkupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya. Kenako tinaima ku Turo kuti katundu atsitsidwe mʼngalawa. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 173-175
3 Chilumba cha Kupuro chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere* nʼkupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya. Kenako tinaima ku Turo kuti katundu atsitsidwe mʼngalawa.