Machitidwe 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chilumba cha Kupuro+ chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere ndi kupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya.+ Tinaima ku Turo, chifukwa kumeneko ngalawa inafunika kutsitsa katundu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 173-175
3 Chilumba cha Kupuro+ chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere ndi kupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya.+ Tinaima ku Turo, chifukwa kumeneko ngalawa inafunika kutsitsa katundu.+