Machitidwe 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, komabe anamuuza kuti: “Mʼbale, pali Ayuda ambiri okhulupirira ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 182-183 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, ptsa. 23-2410/15/2002, tsa. 30
20 Iwo atamva zimenezi anayamba kutamanda Mulungu, komabe anamuuza kuti: “Mʼbale, pali Ayuda ambiri okhulupirira ndipo onsewa ndi odzipereka pa nkhani yotsatira Chilamulo.+
21:20 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 182-183 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, ptsa. 23-2410/15/2002, tsa. 30