Aroma 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse amene anachimwa asakudziwa Chilamulo, adzafa asakudziwa Chilamulo.+ Koma onse amene anachimwa akudziwa Chilamulo, adzaweruzidwa mogwirizana ndi Chilamulocho.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 10
12 Anthu onse amene anachimwa asakudziwa Chilamulo, adzafa asakudziwa Chilamulo.+ Koma onse amene anachimwa akudziwa Chilamulo, adzaweruzidwa mogwirizana ndi Chilamulocho.+