-
Aroma 5:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pali kusiyananso pakati pa mphatso yaulereyi ndi mmene zinthu zinachitikira kudzera mwa munthu mmodzi amene anachimwa.+ Chiweruzo cha tchimo limodzi lija chinabweretsa uchimo kwa onse,+ koma mphatso imene inaperekedwa chifukwa cha machimo ambiri, inachititsa kuti anthu azionedwa kuti ndi olungama.+
-