Aroma 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu sanakane anthu ake amene anali oyambirira kuwavomereza.+ Kodi simukudziwa zimene lemba lina limanena zokhudza Eliya, pamene anachonderera Mulungu motsutsa Aisiraeli? Limati: Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Galamukani!,7/8/1990, tsa. 13
2 Mulungu sanakane anthu ake amene anali oyambirira kuwavomereza.+ Kodi simukudziwa zimene lemba lina limanena zokhudza Eliya, pamene anachonderera Mulungu motsutsa Aisiraeli? Limati: