Aroma 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu sanakane anthu ake amene anali oyambirira kuwavomereza.+ Kodi ndithu simukudziwa kuti Lemba limati chiyani za Eliya, pamene anali kuchonderera Mulungu motsutsa Aisiraeli?+ Limati: Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Galamukani!,7/8/1990, tsa. 13
2 Mulungu sanakane anthu ake amene anali oyambirira kuwavomereza.+ Kodi ndithu simukudziwa kuti Lemba limati chiyani za Eliya, pamene anali kuchonderera Mulungu motsutsa Aisiraeli?+ Limati: