Aroma 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova,* iwo apha aneneri anu ndipo agwetsa maguwa anu ansembe moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano ayambanso kundifunafuna kuti andiphe.”+
3 “Yehova,* iwo apha aneneri anu ndipo agwetsa maguwa anu ansembe moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano ayambanso kundifunafuna kuti andiphe.”+