Aroma 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova, iwo apha aneneri anu, agumula maguwa anu ansembe, moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano akufunafuna moyo wanga.”+
3 “Yehova, iwo apha aneneri anu, agumula maguwa anu ansembe, moti ine ndatsala ndekhandekha. Tsopano akufunafuna moyo wanga.”+