Aroma 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kulakwa kwawo kwabweretsa chuma mʼdziko ndipo kuchepa kwawo kukutanthauza chuma kwa anthu a mitundu ina.+ Choncho padzakhala madalitso ambiri chiwerengero chawo chikadzakwanira.
12 Kulakwa kwawo kwabweretsa chuma mʼdziko ndipo kuchepa kwawo kukutanthauza chuma kwa anthu a mitundu ina.+ Choncho padzakhala madalitso ambiri chiwerengero chawo chikadzakwanira.