Aroma 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungu walola onse kuti akhale akaidi a kusamvera+ kuti onsewo awasonyeze chifundo.+