Aroma 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense, kupatulapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa lamulo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:8 Galamukani!,4/8/1999, ptsa. 16-17
8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense, kupatulapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa lamulo.+