Aroma 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho abale, ndikukupemphani kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu komanso chikondi cha mzimu, kuti muzilimbikira kundipempherera kwa Mulungu ndipo nanenso ndikulimbikira kupemphera.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:30 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 53/15/2001, tsa. 31
30 Choncho abale, ndikukupemphani kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu komanso chikondi cha mzimu, kuti muzilimbikira kundipempherera kwa Mulungu ndipo nanenso ndikulimbikira kupemphera.+