Aroma 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:30 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 53/15/2001, tsa. 31
30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+