2 Akorinto 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inunso mungathandizepo mwa kutiperekera mapembedzero anu,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira+ zinthu zimene tapatsidwa mokoma mtima, chifukwa cha mapemphero a anthu ambiri.+ Aefeso 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene mukutero, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ mwa mtundu uliwonse wa pemphero+ ndi pembedzero. Kuti muchite zimenezi, khalani maso mosalekeza ndi kupemphera mopembedzera m’malo mwa oyera onse, Akolose 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muzitipemphereranso ifeyo,+ kuti Mulungu atitsegulire khomo+ kuti tithe kulalikira mawu ndi kulankhula za chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu, chimene ndinamangidwira n’kukhala m’ndende muno,+ 1 Atesalonika 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Abale, pitirizani kutipempherera.+
11 Inunso mungathandizepo mwa kutiperekera mapembedzero anu,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira+ zinthu zimene tapatsidwa mokoma mtima, chifukwa cha mapemphero a anthu ambiri.+
18 Pamene mukutero, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ mwa mtundu uliwonse wa pemphero+ ndi pembedzero. Kuti muchite zimenezi, khalani maso mosalekeza ndi kupemphera mopembedzera m’malo mwa oyera onse,
3 Muzitipemphereranso ifeyo,+ kuti Mulungu atitsegulire khomo+ kuti tithe kulalikira mawu ndi kulankhula za chinsinsi chopatulika+ chonena za Khristu, chimene ndinamangidwira n’kukhala m’ndende muno,+