Mateyu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera. Yuda 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma inu okondedwa, podzilimbitsa+ pamaziko a chikhulupiriro chanu choyera kopambana,+ ndi kupemphera mu mphamvu ya mzimu woyera,+
6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.
20 Koma inu okondedwa, podzilimbitsa+ pamaziko a chikhulupiriro chanu choyera kopambana,+ ndi kupemphera mu mphamvu ya mzimu woyera,+