Aroma 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+ Afilipi 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 chifukwa ndikudziwa kuti mwa mapembedzero+ anu, ndi mwa mzimu wa Yesu Khristu,+ ndidzamasulidwa. Filimoni 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni.
30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+
22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni.