-
Machitidwe 28:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Pamenepo iwo anapangana naye tsiku, ndipo anabwera mwaunyinji kumene iye anali kukhala. Chotero kuyambira m’mawa mpaka madzulo, anawafotokozera nkhani yonse pochitira umboni mokwanira za ufumu wa Mulungu.+ Anachitira umboniwo mwa kugwiritsa ntchito mfundo zokopa zokhudza Yesu, kuchokera m’chilamulo cha Mose+ ndi mu Zolemba za aneneri.+
-