2 Akorinto 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inunso mungathandizepo potipempherera mochonderera,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira thandizo limene Mulungu amatipatsa poyankha mapemphero a anthu ambiri.+
11 Inunso mungathandizepo potipempherera mochonderera,+ kuti pakhale anthu ambiri otiperekera mapemphero oyamikira thandizo limene Mulungu amatipatsa poyankha mapemphero a anthu ambiri.+