1 Akorinto 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwa nzeru zake, Mulungu sanalole kuti dziko ligwiritse ntchito nzeru zake+ pomudziwa.+ Mʼmalomwake, Mulungu anaona kuti ndi bwino kupulumutsa okhulupirira kudzera mu uthenga umene anthu ena amauona kuti ndi wopusa.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, tsa. 269/15/1992, ptsa. 19-24
21 Mwa nzeru zake, Mulungu sanalole kuti dziko ligwiritse ntchito nzeru zake+ pomudziwa.+ Mʼmalomwake, Mulungu anaona kuti ndi bwino kupulumutsa okhulupirira kudzera mu uthenga umene anthu ena amauona kuti ndi wopusa.+