1 Akorinto 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa chinthu cha Mulungu chimene anthu amachiona kuti nʼchopusa, nʼchanzeru kuposa anthu. Ndipo chinthu cha Mulungu chimene anthu amachiona kuti nʼchofooka, nʼchamphamvu kuposa anthu.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:25 Kukambitsirana, tsa. 139
25 Chifukwa chinthu cha Mulungu chimene anthu amachiona kuti nʼchopusa, nʼchanzeru kuposa anthu. Ndipo chinthu cha Mulungu chimene anthu amachiona kuti nʼchofooka, nʼchamphamvu kuposa anthu.+