6 Tsopano abale, ndanena zinthu zimenezi zokhudza ineyo ndi Apolo+ kuti mumvetse mfundo yake nʼcholinga choti muphunzire kwa ife lamulo lakuti: “Musapitirire zinthu zolembedwa.” Sitikufuna kuti aliyense wa inu akhale wodzikuza+ nʼkumachita zinthu mokondera.