1 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mulungu anaukitsa Ambuye+ ndipo adzaukitsanso ifeyo+ pogwiritsa ntchito mphamvu zake.+