1 Akorinto 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe si onse amene amadziwa zimenezi.+ Ena, chifukwa choti poyamba ankalambira mafano, akamadya chakudya choperekedwa kwa mafano amachiona ngati choperekedwadi kwa mafano.+ Kenako chikumbumtima chawo chimawavutitsa popeza nʼchofooka.+
7 Komabe si onse amene amadziwa zimenezi.+ Ena, chifukwa choti poyamba ankalambira mafano, akamadya chakudya choperekedwa kwa mafano amachiona ngati choperekedwadi kwa mafano.+ Kenako chikumbumtima chawo chimawavutitsa popeza nʼchofooka.+