7 Ngakhale zili choncho, si onse amene amadziwa zimenezi.+ Koma ena, pokhala ozolowera mafano enaake mpaka panopo, akamadya chakudya choperekedwa kwa fano amachidya monga choperekedwadi kwa fano,+ ndipo popeza chikumbumtima chawo n’chofooka, chimaipitsidwa.+