Aroma 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikudziwa ndipo ndikukhulupirira mwa Ambuye Yesu kuti palibe chakudya chodetsedwa mwa icho chokha.+ Koma ngati munthu akuona chinachake monga chodetsedwa, kwa iyeyo ndi chodetsedwa.+ 1 Akorinto 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati wina mwa osakhulupirira wakuitanani ndipo mwapita, kadyeni zonse zimene wakupatsani,+ popanda kufunsa mafunso poopera chikumbumtima chanu.+
14 Ndikudziwa ndipo ndikukhulupirira mwa Ambuye Yesu kuti palibe chakudya chodetsedwa mwa icho chokha.+ Koma ngati munthu akuona chinachake monga chodetsedwa, kwa iyeyo ndi chodetsedwa.+
27 Ngati wina mwa osakhulupirira wakuitanani ndipo mwapita, kadyeni zonse zimene wakupatsani,+ popanda kufunsa mafunso poopera chikumbumtima chanu.+