Mateyu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+ Machitidwe 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+ 1 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+
11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+
15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+
4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+