1 Akorinto 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi ndilibe ufulu wochita zimene ndikufuna? Kodi si ine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu si ntchito yanga mwa Ambuye?
9 Kodi ndilibe ufulu wochita zimene ndikufuna? Kodi si ine mtumwi? Kodi sindinaone Yesu Ambuye wathu?+ Kodi inu si ntchito yanga mwa Ambuye?