-
Machitidwe 9:3-5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ali pa ulendo wakewo, atatsala pangʼono kufika ku Damasiko, mwadzidzidzi anangoona kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+ 4 Zitatero anagwa pansi ndipo anamva mawu akuti: “Saulo, Saulo, nʼchifukwa chiyani ukundizunza?” 5 Iye anafunsa kuti: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu,+ amene ukumuzunza.+
-