1 Akorinto 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati anthu ena amayembekezera kuti muwachitire zimenezi, ndiye kuli bwanji ifeyo? Komatu ife sitinagwiritse ntchito ufulu umenewo.+ Koma timapirira zinthu zonse kuti tisalepheretse ena kumva uthenga wabwino wonena za Khristu.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, ptsa. 25-27
12 Ngati anthu ena amayembekezera kuti muwachitire zimenezi, ndiye kuli bwanji ifeyo? Komatu ife sitinagwiritse ntchito ufulu umenewo.+ Koma timapirira zinthu zonse kuti tisalepheretse ena kumva uthenga wabwino wonena za Khristu.+