1 Akorinto 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukhale ndi chikondi koma muziyesetsanso kuti mulandire mphatso za mzimu woyera, makamaka mphatso ya kunenera.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,10/15/1993, tsa. 31
14 Mukhale ndi chikondi koma muziyesetsanso kuti mulandire mphatso za mzimu woyera, makamaka mphatso ya kunenera.+