1 Akorinto 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Nsanja ya Olonda,10/15/1993, tsa. 31
14 Yesetsani kukhala ndi chikondi, komanso pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zauzimu,+ makamaka kunenera.+