1 Akorinto 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa wolankhula malilime* salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu. Palibe amene amamva zonena zake,+ koma iye amalankhula zinsinsi zopatulika+ mothandizidwa ndi mzimu.
2 Chifukwa wolankhula malilime* salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu. Palibe amene amamva zonena zake,+ koma iye amalankhula zinsinsi zopatulika+ mothandizidwa ndi mzimu.