6 Abale, kodi mungapindule chiyani ngati pa nthawi ino nditabwera kwa inu ndikulankhula malilime amene simukuwadziwa? Zingakhale zothandiza ngati ndingabwere ndi mawu amene ndalandira kuchokera kwa Mulungu,+ kapena mphatso yodziwa zinthu,+ kapena ulosi kapenanso chiphunzitso.