1 Akorinto 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amadziwa zinthu zobisika zamumtima mwake, moti adzawerama nʼkulambira Mulungu, ndi kunena kuti: “Zoonadi Mulungu ali pakati panu.”+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:25 Nsanja ya Olonda,11/15/1988, ptsa. 15-16, 20
25 Amadziwa zinthu zobisika zamumtima mwake, moti adzawerama nʼkulambira Mulungu, ndi kunena kuti: “Zoonadi Mulungu ali pakati panu.”+