1 Akorinto 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati pali anthu olankhula malilime,* asapose awiri kapena atatu ndipo azipatsana mpata komanso wina azimasulira.+
27 Ngati pali anthu olankhula malilime,* asapose awiri kapena atatu ndipo azipatsana mpata komanso wina azimasulira.+