1 Akorinto 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo ngati pali anthu olankhula lilime lachilendo, asapose awiri kapena atatu, azisiyirana mpata, ndipo wina amasulire.+
27 Ndipo ngati pali anthu olankhula lilime lachilendo, asapose awiri kapena atatu, azisiyirana mpata, ndipo wina amasulire.+