1 Akorinto 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aneneri+ awiri kapena atatu alankhule, ndipo ena onse aziyesetsa kumvetsa tanthauzo la zimene iwo akulankhulazo.
29 Aneneri+ awiri kapena atatu alankhule, ndipo ena onse aziyesetsa kumvetsa tanthauzo la zimene iwo akulankhulazo.