1 Akorinto 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ponena za mʼbale wathu Apolo,+ ndinamuchonderera kwambiri kuti abwere kwanuko pamodzi ndi abale. Sichinali cholinga chake kuti abwere panopa, koma adzabwera akadzapeza mpata. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:12 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 22
12 Ponena za mʼbale wathu Apolo,+ ndinamuchonderera kwambiri kuti abwere kwanuko pamodzi ndi abale. Sichinali cholinga chake kuti abwere panopa, koma adzabwera akadzapeza mpata.