1 Akorinto 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano kunena za m’bale wathu Apolo,+ ndinamuchonderera kwambiri kuti abwere kwanuko pamodzi ndi abale, koma iye sanafune kubwera pa nthawi ino. Adzabwera akadzapeza mpata. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:12 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 22
12 Tsopano kunena za m’bale wathu Apolo,+ ndinamuchonderera kwambiri kuti abwere kwanuko pamodzi ndi abale, koma iye sanafune kubwera pa nthawi ino. Adzabwera akadzapeza mpata.