2 Akorinto 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiponso pali mgwirizano wotani pakati pa Khristu ndi Beliyali?*+ Nanga munthu wokhulupirira* ndi wosakhulupirira angafanane pa zinthu ziti?+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, ptsa. 18-22
15 Ndiponso pali mgwirizano wotani pakati pa Khristu ndi Beliyali?*+ Nanga munthu wokhulupirira* ndi wosakhulupirira angafanane pa zinthu ziti?+