2 Akorinto 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho tinalimbikitsa Tito+ kuti, popeza iye ndi amene anayambitsa ntchito yotolera zopereka zanu, iyeyo amalizitsenso kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:6 Nsanja ya Olonda,11/15/1998, tsa. 30
6 Choncho tinalimbikitsa Tito+ kuti, popeza iye ndi amene anayambitsa ntchito yotolera zopereka zanu, iyeyo amalizitsenso kusonkhanitsa mphatso zanu zachifundo.