7 Inuyo mukuchita bwino pa chilichonse. Chikhulupiriro chanu ndi cholimba, muli ndi luso la kulankhula, mumadziwa zambiri, mumachita zinthu zonse mwakhama ndiponso mumakonda ena mmene ife timakukonderani. Choncho pitirizaninso kukhala ndi mtima wofuna kupereka.+