7 Inuyo mukusefukira mu ntchito+ monga chikhulupiriro, kudziwa kulankhula, kudziwa zinthu,+ khama pa zonse zimene mumachita, ndipo mumasonyeza chikondi chofanana ndi chimene tili nacho pa inu. Chotero musefukirenso chimodzimodzi pa nkhani ya kupereka kumene tikunenaku.