-
2 Akorinto 8:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Abalewa tikuwatumizanso limodzi ndi mʼbale wathu amene tamuyesa mobwerezabwereza ndipo taona kuti ndi wakhama pa zinthu zambiri. Panopa wasonyezanso kuti ndi wakhama kwambiri chifukwa akukukhulupirirani kwambiri.
-