-
2 Akorinto 8:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pamodzi ndi abalewo, tatumizanso m’bale wathu amene mobwerezabwereza tamuona kuti ndi wakhama pa zinthu zambiri, ndipo tsopano wawonjezera khama lake chifukwa akukukhulupirirani kwambiri.
-