2 Akorinto 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho asonyezeni kuti mumawakonda+ ndiponso musonyeze mipingo chifukwa chake timakunyadirani.